"Mwina mmodzi mwa adani aakulu omwe mutha kukumana nawo ndi 'woneneza pakati pa abale'." Landirani chidziwitso chachikulu cha momwe chida chimenechi cha kuneneza chimadzera ndipo phunzirani za momwe mungachigonjetsere, pomwe mukuwerenga bukhu lapamwambali, lolembedwa ndi Dag Heward-Mills.